Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 36:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova Mulungu wa makolo awo anapitiriza kuwatumizira machenjezo kudzera mwa amithenga ake.+ Anawatumiza mobwerezabwereza chifukwa ankamvera chisoni anthu akewo+ ndiponso malo ake okhala.+

  • Miyambo 1:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Popeza ndaitana koma inu mukupitiriza kukana,+ ndatambasula dzanja langa koma palibe amene akumvetsera,+

  • Yesaya 50:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 N’chifukwa chiyani nditabwera sindinapeze aliyense?+ N’chifukwa chiyani nditaitana palibe amene anayankha?+ Kodi dzanja langa lafupika kwambiri moti silingathe kuwombola,+ kapena kodi mwa ine mulibe mphamvu zopulumutsira? Inetu ndimaumitsa nyanja+ pongoidzudzula chabe.+ Mitsinje ndimaisandutsa chipululu.+ Nsomba zake zimanunkha chifukwa chakuti mulibe madzi ndipo zimafa ndi ludzu.+

  • Yesaya 66:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ineyo ndidzasankha njira zowazunzira.+ Ndidzawabweretsera zinthu zimene amachita nazo mantha+ chifukwa ndinaitana koma palibe amene anayankha. Ndinalankhula koma palibe amene anamvera.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zoipa pamaso panga ndipo anasankha zinthu zimene sindisangalala nazo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena