Yesaya 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Tsopano lemba zimenezi pacholembapo, iwo akuona. Uzilembe m’buku+ kuti m’tsogolo zidzakhale umboni mpaka kalekale.+ Habakuku 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Yehova anandiyankha kuti: “Lemba masomphenyawa moonekera bwino pamiyala yosema,+ kuti wowerenga mokweza awerenge mosadodoma.+
8 “Tsopano lemba zimenezi pacholembapo, iwo akuona. Uzilembe m’buku+ kuti m’tsogolo zidzakhale umboni mpaka kalekale.+
2 Pamenepo Yehova anandiyankha kuti: “Lemba masomphenyawa moonekera bwino pamiyala yosema,+ kuti wowerenga mokweza awerenge mosadodoma.+