Yesaya 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Tsopano pita ukalembe zimenezi pacholembapo, iwo akuona.Ndipo ukazilembe mʼbuku+Kuti mʼtsogoloZidzakhale umboni mpaka kalekale.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:8 Yesaya 1, tsa. 304
8 “Tsopano pita ukalembe zimenezi pacholembapo, iwo akuona.Ndipo ukazilembe mʼbuku+Kuti mʼtsogoloZidzakhale umboni mpaka kalekale.+