Oweruza 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anayamba kusankha milungu yatsopano.+Atatero m’pamene nkhondo inafika m’mizinda.+Panalibe chishango kapena mkondo waung’ono,Pakati pa anthu 40,000 mu Isiraeli.+ Salimo 81:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho ndinawasiya kuti apitirize kuumitsa mtima wawo.+Iwo anapitiriza kuyenda mu nzeru zawo.+ Yeremiya 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ponena za anthu awa Yehova wati: “Iwo akukonda kuyendayenda+ ndipo sanalamulire mapazi awo.+ Choncho Yehova sakukondwera nawo,+ moti adzakumbukira zolakwa zawo ndipo adzawalanga chifukwa cha machimo awo.”+
8 Anayamba kusankha milungu yatsopano.+Atatero m’pamene nkhondo inafika m’mizinda.+Panalibe chishango kapena mkondo waung’ono,Pakati pa anthu 40,000 mu Isiraeli.+
10 Ponena za anthu awa Yehova wati: “Iwo akukonda kuyendayenda+ ndipo sanalamulire mapazi awo.+ Choncho Yehova sakukondwera nawo,+ moti adzakumbukira zolakwa zawo ndipo adzawalanga chifukwa cha machimo awo.”+