Levitiko 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ena mwa magaziwo aziwapaka panyanga za guwa lansembe+ limene lili pamaso pa Yehova, m’chihema chokumanako. Magazi ena onse aziwathira pansi pa guwa lansembe zopsereza,+ limene lili pakhomo la chihema chokumanako. Levitiko 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti moyo wa nyama uli m’magazi+ ndipo ine ndakuikirani magazi paguwa lansembe kuti azikuphimbirani machimo.+ Zili choncho popeza magazi+ ndiwo amaphimba machimo,+ chifukwa moyo uli m’magaziwo.
18 Ena mwa magaziwo aziwapaka panyanga za guwa lansembe+ limene lili pamaso pa Yehova, m’chihema chokumanako. Magazi ena onse aziwathira pansi pa guwa lansembe zopsereza,+ limene lili pakhomo la chihema chokumanako.
11 Pakuti moyo wa nyama uli m’magazi+ ndipo ine ndakuikirani magazi paguwa lansembe kuti azikuphimbirani machimo.+ Zili choncho popeza magazi+ ndiwo amaphimba machimo,+ chifukwa moyo uli m’magaziwo.