Salimo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mudzasangalatsadi mtima wanga,+Kuposanso mmene iwo amasangalalira, mbewu ndi vinyo wawo watsopano zikachuluka.+ Salimo 126:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amene akupita kumunda akulira,+Atasenza thumba lodzaza mbewu,+Adzabwerako akufuula mosangalala,+Atasenza mtolo wake wa zokolola.+
7 Mudzasangalatsadi mtima wanga,+Kuposanso mmene iwo amasangalalira, mbewu ndi vinyo wawo watsopano zikachuluka.+
6 Amene akupita kumunda akulira,+Atasenza thumba lodzaza mbewu,+Adzabwerako akufuula mosangalala,+Atasenza mtolo wake wa zokolola.+