Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Samala mayendedwe+ ako ukapita kunyumba ya Mulungu woona. Ukapita kumeneko uzikamvetsera,+ osati uzikapereka nsembe monga mmene amachitira anthu opusa,+ pakuti iwo sadziwa kuti akuchita zoipa.+

  • Malaki 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mukapereka nsembe nyama yakhungu, mumanena kuti: “Palibe cholakwika.” Mukapereka nsembe nyama yolumala kapena yodwala, mumanena kuti: “Palibe cholakwika.”’”+

      “Pitani nayo kwa bwanamkubwa wanu. Kodi akakondwera nanu? Kapena kodi akakulandirani bwino?” watero Yehova wa makamu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena