Salimo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti inu sindinu Mulungu wokondwera ndi zoipa,+Palibe munthu woipa amene angakhale ndi inu ngakhale kwa kanthawi kochepa.+ Salimo 147:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye sadalira mphamvu za hatchi,+Kapena liwiro la miyendo ya munthu.+
4 Pakuti inu sindinu Mulungu wokondwera ndi zoipa,+Palibe munthu woipa amene angakhale ndi inu ngakhale kwa kanthawi kochepa.+