1 Mbiri 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Yamikani Yehova,+ anthu inu. Itanani pa dzina lake.+Dziwitsani mitundu ya anthu ntchito zake!+ Salimo 105:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 105 YAMIKANI Yehova, itanani pa dzina lake,+Lengezani zochita zake pakati pa mitundu ya anthu.+ Aroma 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti “aliyense amene adzaitana pa dzina la Yehova* adzapulumuka.”+