Yesaya 47:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Umu ndi mmene amatsenga+ ako amene wawavutikira kuyambira uli mwana adzakhalire. Iwo adzabalalika, aliyense kulowera kuchigawo cha kwawo ndipo sipadzakhala woti akupulumutse.+
15 Umu ndi mmene amatsenga+ ako amene wawavutikira kuyambira uli mwana adzakhalire. Iwo adzabalalika, aliyense kulowera kuchigawo cha kwawo ndipo sipadzakhala woti akupulumutse.+