Genesis 41:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kutacha m’mawa, Farao anavutika kwambiri ndi maganizo.+ Chotero anaitanitsa ansembe onse amatsenga+ ndi amuna anzeru+ onse a mu Iguputo, n’kuwafotokozera maloto akewo.+ Koma palibe amene anatha kum’masulira Farao malotowo. 1 Mafumu 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Nzeru za Solomo zinaposa+ nzeru za anthu onse a Kum’mawa+ ndi nzeru zonse za ku Iguputo.+ Mlaliki 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Zonsezi ndinazifufuza mwanzeru ndipo ndinati: “Ndidzakhala wanzeru.” Koma nzeruzo zinatalikirana nane.+ Machitidwe 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chotero Mose anaphunzira nzeru+ zonse za Aiguputo. Ndipo anali wamphamvu m’mawu+ ndi m’zochita zake.
8 Kutacha m’mawa, Farao anavutika kwambiri ndi maganizo.+ Chotero anaitanitsa ansembe onse amatsenga+ ndi amuna anzeru+ onse a mu Iguputo, n’kuwafotokozera maloto akewo.+ Koma palibe amene anatha kum’masulira Farao malotowo.
23 Zonsezi ndinazifufuza mwanzeru ndipo ndinati: “Ndidzakhala wanzeru.” Koma nzeruzo zinatalikirana nane.+
22 Chotero Mose anaphunzira nzeru+ zonse za Aiguputo. Ndipo anali wamphamvu m’mawu+ ndi m’zochita zake.