Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+

  • Ezekieli 34:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Nkhosazo komanso malo ozungulira phiri langa ndidzawasandutsa dalitso.+ Ndidzagwetsa mvula yambiri pa nthawi yake. Kudzagwa mvula yambiri yamadalitso.+

  • Zekariya 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Monga mmene munakhalira temberero pakati pa anthu a mitundu ina,+ inu a nyumba ya Yuda ndi a nyumba ya Isiraeli,+ ndidzakupulumutsani ndipo mudzakhala dalitso.+ Musachite mantha.+ Limbani mtima ndipo mukonzeke kugwira ntchito.’+

  • Agalatiya 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Cholinga chake chinali chakuti mitundu ipeze madalitso amene Abulahamu analonjezedwa kudzera mwa Yesu Khristu,+ kuti tidzalandire mzimu wolonjezedwawo+ chifukwa cha chikhulupiriro chathu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena