Yesaya 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mafumu ena onse a mitundu ya anthu anagona pansi mu ulemerero, aliyense m’manda ake.+ Mateyu 27:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 ndipo anakauika m’manda ake achikumbutso atsopano,+ amene anawasema m’thanthwe. Kenako anagubuduza chimwala chachikulu ndi kutseka pakhomo la manda achikumbutsowo, n’kuchoka.+
60 ndipo anakauika m’manda ake achikumbutso atsopano,+ amene anawasema m’thanthwe. Kenako anagubuduza chimwala chachikulu ndi kutseka pakhomo la manda achikumbutsowo, n’kuchoka.+