Deuteronomo 29:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mitundu yonse idzanena kuti, ‘N’chifukwa chiyani Yehova wachitira dzikoli zimenezi?+ N’chifukwa chiyani mkwiyo wake wayaka kwambiri chonchi?’ Salimo 94:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nyamukani inu Woweruza dziko lapansi.+Perekani chilango kwa anthu odzikweza.+
24 Mitundu yonse idzanena kuti, ‘N’chifukwa chiyani Yehova wachitira dzikoli zimenezi?+ N’chifukwa chiyani mkwiyo wake wayaka kwambiri chonchi?’