Deuteronomo 32:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kodi sindinasunge zimenezi,Ndi kuziikira chidindo m’nkhokwe yanga?+ Yobu 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kulakwa kwanga mwakutsekera m’thumba,+Ndipo mwamata machimo anga ndi zomatira. Salimo 90:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zolakwa zathu mwaziika patsogolo panu,+Ndipo machimo athu obisika* ali patsogolo pa nkhope yanu yowala.+ Yeremiya 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti maso anga akuona njira zawo zonse. Anthuwo sanabisike kwa ine, ndipo zolakwa zawo sizinabisike pamaso panga.+ Hoseya 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Zolakwa za Efuraimu zakulungidwa pamodzi, ndipo machimo ake asungidwa.+ Amosi 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Yehova, amene ndi ulemerero wa Yakobo, walumbira pa dzina lake+ kuti, ‘Sindidzaiwala ntchito zawo zonse.+
8 Zolakwa zathu mwaziika patsogolo panu,+Ndipo machimo athu obisika* ali patsogolo pa nkhope yanu yowala.+
17 Pakuti maso anga akuona njira zawo zonse. Anthuwo sanabisike kwa ine, ndipo zolakwa zawo sizinabisike pamaso panga.+
7 “Yehova, amene ndi ulemerero wa Yakobo, walumbira pa dzina lake+ kuti, ‘Sindidzaiwala ntchito zawo zonse.+