Salimo 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amene akufunafuna moyo wanga achite manyazi ndi kunyozeka.+Amene akundikonzera chiwembu muwabweze ndipo athedwe nzeru.+ Salimo 59:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova, Mulungu wa makamu, ndinu Mulungu wa Isiraeli.+Nyamukani ndi kuweruza mitundu yonse ya anthu.+Musakomere mtima aliyense woipa ndi wachiwembu.+ [Seʹlah.] Salimo 109:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova akumbukire cholakwa cha makolo ake,+Ndipo tchimo la mayi ake+ lisafafanizidwe.+
4 Amene akufunafuna moyo wanga achite manyazi ndi kunyozeka.+Amene akundikonzera chiwembu muwabweze ndipo athedwe nzeru.+
5 Inu Yehova, Mulungu wa makamu, ndinu Mulungu wa Isiraeli.+Nyamukani ndi kuweruza mitundu yonse ya anthu.+Musakomere mtima aliyense woipa ndi wachiwembu.+ [Seʹlah.]