Salimo 48:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pogwiritsa ntchito mphepo yamphamvu ya kum’mawa, munaswa zombo za ku Tarisi.+ Yeremiya 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho ndidzakumwazani+ ngati mapesi amene akuuluka ndi mphepo kuchokera m’chipululu.+