Salimo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma oipa sali choncho.Iwo ali ngati mankhusu* amene amauluzika ndi mphepo.+ Yeremiya 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa nthawiyo adzauza anthu awa ndi Yerusalemu kuti: “M’njira zodutsidwadutsidwa za m’chipululu zopita kwa mwana wamkazi wa anthu anga+ mukutuluka mphepo yotentha.+ Mphepo imeneyi si youluzira mankhusu* kapena yoyeretsera tirigu. Hoseya 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero iwo adzakhala ngati mitambo ya m’mawa+ ndiponso ngati mame amene sachedwa kuuma. Adzakhalanso ngati mankhusu* amene amauluzika kuchokera pamalo opunthira mbewu+ ndiponso ngati utsi umene umatuluka m’chumuni kudenga.*
11 Pa nthawiyo adzauza anthu awa ndi Yerusalemu kuti: “M’njira zodutsidwadutsidwa za m’chipululu zopita kwa mwana wamkazi wa anthu anga+ mukutuluka mphepo yotentha.+ Mphepo imeneyi si youluzira mankhusu* kapena yoyeretsera tirigu.
3 Chotero iwo adzakhala ngati mitambo ya m’mawa+ ndiponso ngati mame amene sachedwa kuuma. Adzakhalanso ngati mankhusu* amene amauluzika kuchokera pamalo opunthira mbewu+ ndiponso ngati utsi umene umatuluka m’chumuni kudenga.*