2 Mafumu 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tcherani khutu lanu, inu Yehova, mumve.+ Tsegulani maso anu,+ inu Yehova, muone, ndipo imvani mawu a Senakeribu amene watumiza kudzatonza nawo+ Mulungu wamoyo. Nehemiya 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Nehemiya anati: “Inu Mulungu wathu, imvani+ mawu onyoza amene akutinenera.+ Bwezerani chitonzo chawocho+ pamutu pawo ndipo apititseni m’dziko laukapolo monga zofunkha.
16 Tcherani khutu lanu, inu Yehova, mumve.+ Tsegulani maso anu,+ inu Yehova, muone, ndipo imvani mawu a Senakeribu amene watumiza kudzatonza nawo+ Mulungu wamoyo.
4 Ndiyeno Nehemiya anati: “Inu Mulungu wathu, imvani+ mawu onyoza amene akutinenera.+ Bwezerani chitonzo chawocho+ pamutu pawo ndipo apititseni m’dziko laukapolo monga zofunkha.