Salimo 38:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu amene akufuna kundiwononga anditchera misampha,+Amene akufuna kundivulaza akulankhula motsutsana nane,+Ndipo amakhala akukonza zachinyengo tsiku lonse.+ Salimo 64:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amaumirira kulankhula zoipa,+Amakambirana kuti atchere misampha.+Iwo amati: “Angaione ndani?”+ Salimo 140:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu odzikweza anditchera msampha.+Iwo aika zingwe ponseponse ngati ukonde m’mphepete mwa njira,+Ndipo anditchera makhwekhwe.+ [Seʹlah.]
12 Anthu amene akufuna kundiwononga anditchera misampha,+Amene akufuna kundivulaza akulankhula motsutsana nane,+Ndipo amakhala akukonza zachinyengo tsiku lonse.+
5 Anthu odzikweza anditchera msampha.+Iwo aika zingwe ponseponse ngati ukonde m’mphepete mwa njira,+Ndipo anditchera makhwekhwe.+ [Seʹlah.]