Salimo 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mumtima mwake+ amanena kuti: “Mulungu waiwala zochita zanga.+Wabisa nkhope yake.+Ndithudi, sadzaona kalikonse.”+ Salimo 59:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Taonani! Amabwetuka ndi pakamwa pawo.+Milomo yawo ili ngati malupanga,+Pakuti iwo amati: “Ndani akumvetsera?”+ Salimo 94:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo amanena kuti: “Ya sakuona,+Ndipo Mulungu wa Yakobo sakudziwa zimene zikuchitika.”+ Ezekieli 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi waona zimene akuluakulu a Isiraeli akuchita mu mdima?+ Kodi waona zimene aliyense wa iwo akuchita m’chipinda chamkati mmene muli fano lake losema? Iwo akunena kuti, ‘Yehova sakutiona.+ Yehova wachokamo m’dziko muno.’”
11 Mumtima mwake+ amanena kuti: “Mulungu waiwala zochita zanga.+Wabisa nkhope yake.+Ndithudi, sadzaona kalikonse.”+
7 Taonani! Amabwetuka ndi pakamwa pawo.+Milomo yawo ili ngati malupanga,+Pakuti iwo amati: “Ndani akumvetsera?”+
12 Ndiyeno iye anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi waona zimene akuluakulu a Isiraeli akuchita mu mdima?+ Kodi waona zimene aliyense wa iwo akuchita m’chipinda chamkati mmene muli fano lake losema? Iwo akunena kuti, ‘Yehova sakutiona.+ Yehova wachokamo m’dziko muno.’”