Yeremiya 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 M’mimba mwanga ine, m’mimba mwanga! Ndikumva kupweteka kwambiri mumtima mwanga.+ Mtima wanga ukuvutika.+ Sindingathe kukhala chete pakuti ndamva kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, chizindikiro chochenjeza cha nkhondo.+ Yeremiya 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 M’nyumba zawo mumveke kulira mukawabweretsera magulu achifwamba mwadzidzidzi,+ chifukwa andikumbira mbuna kuti andigwire ndipo anditchera misampha kuti akole mapazi anga.+ Zefaniya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pa tsiku limenelo, lipenga la nyanga ya nkhosa ndiponso chizindikiro chochenjeza zidzalira+ pochenjeza mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, komanso nsanja zazitali kwambiri za m’makona.+
19 M’mimba mwanga ine, m’mimba mwanga! Ndikumva kupweteka kwambiri mumtima mwanga.+ Mtima wanga ukuvutika.+ Sindingathe kukhala chete pakuti ndamva kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, chizindikiro chochenjeza cha nkhondo.+
22 M’nyumba zawo mumveke kulira mukawabweretsera magulu achifwamba mwadzidzidzi,+ chifukwa andikumbira mbuna kuti andigwire ndipo anditchera misampha kuti akole mapazi anga.+
16 Pa tsiku limenelo, lipenga la nyanga ya nkhosa ndiponso chizindikiro chochenjeza zidzalira+ pochenjeza mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, komanso nsanja zazitali kwambiri za m’makona.+