Yeremiya 51:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Ine ndikuthira nkhondo iwe+ phiri lowononga,+ amene wawononga dziko lonse lapansi.+ Ndidzatambasula dzanja langa ndi kukuthira nkhondo. Ndidzakugubuduza kukuchotsa pamatanthwe ndipo ndidzakusandutsa phiri lotenthedwa ndi moto,” watero Yehova.+ Ezekieli 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “‘Pakuti amuna inu mwalankhula zabodza ndipo mwaona masomphenya onama, ine ndithana nanu,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
25 “Ine ndikuthira nkhondo iwe+ phiri lowononga,+ amene wawononga dziko lonse lapansi.+ Ndidzatambasula dzanja langa ndi kukuthira nkhondo. Ndidzakugubuduza kukuchotsa pamatanthwe ndipo ndidzakusandutsa phiri lotenthedwa ndi moto,” watero Yehova.+
8 “‘Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “‘Pakuti amuna inu mwalankhula zabodza ndipo mwaona masomphenya onama, ine ndithana nanu,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”