Chivumbulutso 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako mngelo wachiwiri analiza lipenga lake. Ndipo chinachake chokhala ngati phiri lalikulu+ limene likuyaka moto chinaponyedwa m’nyanja.+ Moti gawo limodzi mwa magawo atatu a nyanja, linasanduka magazi.+ Chivumbulutso 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Mafumu+ a dziko lapansi amene anachita naye dama ndi kusangalala ndi chuma mopanda manyazi, adzalira ndi kudziguguda pachifuwa ndi chisoni chifukwa cha iye,+ poona utsi+ wofuka chifukwa cha kupsa kwake.
8 Kenako mngelo wachiwiri analiza lipenga lake. Ndipo chinachake chokhala ngati phiri lalikulu+ limene likuyaka moto chinaponyedwa m’nyanja.+ Moti gawo limodzi mwa magawo atatu a nyanja, linasanduka magazi.+
9 “Mafumu+ a dziko lapansi amene anachita naye dama ndi kusangalala ndi chuma mopanda manyazi, adzalira ndi kudziguguda pachifuwa ndi chisoni chifukwa cha iye,+ poona utsi+ wofuka chifukwa cha kupsa kwake.