Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Patapita nthawi, mfumu ndi anthu ake anapita ku Yerusalemu kukamenyana ndi Ayebusi+ amene anali kukhala kumeneko. Ayebusiwo anayamba kuuza Davide kuti: “Sulowa mumzinda uno, pakuti upitikitsidwa ndi anthu akhungu ndi olumala.”+ Mumtima mwawo iwo anali kunena kuti: “Davide sangalowe mumzinda uno.”

  • Yeremiya 49:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Bwanji umadzitama chifukwa cha zigwa zako, zigwa zoyenda madzi,+ iwe mwana wamkazi wosakhulupirika? Iwe ukudalira chuma chako,+ ponena kuti: “Ndani angabwere kwa ine?”’”+

  • Maliro 4:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mafumu a padziko lapansi ndiponso anthu onse okhala panthaka ya dziko lapansi,+

      Sanayembekezere kuti mdani angadzalowe pazipata za Yerusalemu.+

  • Obadiya 3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mtima wako wodzikuza wakunyenga,+ iwe amene ukukhala m’malo obisika a m’thanthwe+ pamwamba pa phiri. Iwe ukunena mumtima mwako kuti, ‘Ndani angandigwetsere pansi?’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena