Yeremiya 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Ndakuukira iwe mkazi wokhala m’chigwa,+ iwe mzinda wapathanthwe limene lili pamalo athyathyathya,’ watero Yehova. ‘Koma inu amene mukunena kuti: “Ndani adzabwera kuno kuti atiukire? Ndipo ndani adzalowa m’nyumba zathu?”+ imvani izi,
13 “‘Ndakuukira iwe mkazi wokhala m’chigwa,+ iwe mzinda wapathanthwe limene lili pamalo athyathyathya,’ watero Yehova. ‘Koma inu amene mukunena kuti: “Ndani adzabwera kuno kuti atiukire? Ndipo ndani adzalowa m’nyumba zathu?”+ imvani izi,