Yeremiya 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Taonani! Masiku adzafika,’+ watero Yehova, ‘pamene sadzalumbiranso kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo amene anatulutsa ana a Isiraeli m’dziko la Iguputo!”+
14 “‘Taonani! Masiku adzafika,’+ watero Yehova, ‘pamene sadzalumbiranso kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo amene anatulutsa ana a Isiraeli m’dziko la Iguputo!”+