Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Iye anayamba kuchita uhule chifukwa choona nkhani imeneyi mopepuka. Anali kuipitsa dzikolo+ ndi kuchita chigololo ndi miyala komanso mitengo.+

  • Yeremiya 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndikanakonda kukhala ndi malo a m’chipululu ogona anthu apaulendo.+ Pamenepo ndikanasiya anthu anga ndi kuwachokera, pakuti onsewo ndi achigololo,+ gulu la anthu ochita zachinyengo.+

  • Yeremiya 13:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Chigololo chako,+ kumemesa* kwako,+ khalidwe lako lotayirira la uhule, zonsezi zidzaonekera. Ndaona zinthu zako zonyansa pamapiri kuthengo.+ Tsoka kwa iwe Yerusalemu! Sungakhale woyera.+ Kodi udzakhalabe wosayera kufikira liti?”+

  • Ezekieli 16:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Mkazi amene amachita chigololo amatenga amuna achilendo m’malo mwa mwamuna wake.+

  • Hoseya 7:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Anthu onsewo ndi achigololo.+ Ali ngati ng’anjo yamoto imene wophika mkate waiyatsa. Ng’anjoyo yatentha kwambiri moti iye sakufunikira kuisonkhezera pamene akukanda ufa ndi kudikira kuti ufufume.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena