Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 107:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Nthaka yobala zipatso amaisandutsa dziko lamchere,+

      Chifukwa cha kuipa kwa anthu okhala mmenemo.

  • Yeremiya 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti ndidzalirira mapiri mokweza ndi modandaula+ ndipo ndidzaimba nyimbo yoimba polira, pamene ndikulirira mabusa a m’chipululu. Ndidzalirira zimenezi chifukwa adzakhala atazitentha+ moti palibe munthu amene adzadutsamo. Anthu sadzamva kulira kwa ziweto+ m’mabusamo ndipo zolengedwa zouluka m’mlengalenga ngakhalenso nyama zidzakhala zitathawamo, zitachoka.+

  • Yeremiya 12:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kodi dzikoli lifotabe mpaka liti?+ Kodi zomera za m’minda yonse ziumabe mpaka liti?+ Chifukwa chakuti anthu a m’dzikoli ndi oipa, zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka zinachoka.+ Pakuti anthuwo akuti: “Iye sakuona zimene zidzatichitikira m’tsogolo.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena