Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 8:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kodi iwo anachita manyazi chifukwa anachita zinthu zonyansa?+ Iwo sanachite manyazi ngakhale pang’ono, komanso sanali kudziwa n’komwe kuchita manyazi.+

      “‘Choncho iwo adzagwa pamodzi ndi anthu amene akugwa. Pa nthawi yowalanga+ adzapunthwa,’ watero Yehova.+

  • Yeremiya 11:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndipo sipadzapezeka wotsala pakati pawo, chifukwa ndidzadzetsa tsoka pa anthu a ku Anatoti,+ m’chaka chimene ndidzawapatsa chilango.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena