Salimo 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ubwenzi wolimba ndi Yehova ndi wa anthu amene amamuopa,+Pangano lakenso ndi la anthu oterowo, ndipo iye amawadziwitsa panganolo.+ Salimo 89:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu ayenera kuopedwa pakati pa gulu lake la oyera.+Iye ndi wamkulu ndi wochititsa mantha kuposa onse omuzungulira.+ Yeremiya 23:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ngati iwo akanaima pagulu la anthu amene ndimawakonda,+ akanachititsa anthu anga kumva mawu anga, ndipo akanabweza anthu anga panjira zawo zoipa komanso pa zochita zawo zoipa.”+
14 Ubwenzi wolimba ndi Yehova ndi wa anthu amene amamuopa,+Pangano lakenso ndi la anthu oterowo, ndipo iye amawadziwitsa panganolo.+
7 Mulungu ayenera kuopedwa pakati pa gulu lake la oyera.+Iye ndi wamkulu ndi wochititsa mantha kuposa onse omuzungulira.+
22 Ngati iwo akanaima pagulu la anthu amene ndimawakonda,+ akanachititsa anthu anga kumva mawu anga, ndipo akanabweza anthu anga panjira zawo zoipa komanso pa zochita zawo zoipa.”+