Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 29:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ngati mmene ndinalili m’masiku amene ndinali mnyamata,+

      Pamene Mulungu anali bwenzi langa lapamtima, ndipo anali pahema wanga,+

  • Salimo 15:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Inu Yehova, ndani amene angakhale mlendo m’chihema chanu?+

      Ndani angakhale m’phiri lanu lopatulika?+

  • Salimo 25:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ubwenzi wolimba ndi Yehova ndi wa anthu amene amamuopa,+

      Pangano lakenso ndi la anthu oterowo, ndipo iye amawadziwitsa panganolo.+

  • Yeremiya 23:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndani waimirira pagulu la anthu amene Yehova amawakonda+ kuti azindikire ndi kumva mawu ake?+ Ndani watchera khutu kuti amvetsere mawu ake?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena