Yesaya 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Uwu ndi uthenga wokhudza Babulo,+ umene Yesaya mwana wa Amozi+ anaona m’masomphenya: Yesaya 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 mudzanene mwambi uwu wotonza mfumu ya Babulo: “Uja ankagwiritsa ntchito anzakeyu wasiya ndithu! Wopondereza uja waleka ndithu!+ Yesaya 47:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Tsika ukhale pansi pafumbi+ iwe namwali, mwana wamkazi wa Babulo.+ Khala padothi pomwe palibe mpando wachifumu,+ iwe mwana wamkazi wa Akasidi.+ Pakuti anthu adzaleka kukutchula kuti ndiwe wolekereredwa ndiponso wosasatitsidwa.*+ Yeremiya 51:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Yehova wanena kuti: “Babulo+ pamodzi ndi anthu okhala ku Lebi-kamai ndikuwautsira chimphepo chowononga.+ Danieli 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Kumasulira kwa mawuwa ndi uku: MENE, Mulungu wawerenga masiku a ufumu wanu ndipo waumaliza.+ Danieli 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Usiku womwewo, Belisazara mfumu ya Akasidi anaphedwa,+
4 mudzanene mwambi uwu wotonza mfumu ya Babulo: “Uja ankagwiritsa ntchito anzakeyu wasiya ndithu! Wopondereza uja waleka ndithu!+
47 Tsika ukhale pansi pafumbi+ iwe namwali, mwana wamkazi wa Babulo.+ Khala padothi pomwe palibe mpando wachifumu,+ iwe mwana wamkazi wa Akasidi.+ Pakuti anthu adzaleka kukutchula kuti ndiwe wolekereredwa ndiponso wosasatitsidwa.*+
51 Yehova wanena kuti: “Babulo+ pamodzi ndi anthu okhala ku Lebi-kamai ndikuwautsira chimphepo chowononga.+