Yeremiya 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndipo Zedekiya mfumu ya Yuda sadzapulumuka m’manja mwa Akasidi, pakuti adzaperekedwa ndithu m’manja mwa mfumu ya Babulo moti adzalankhulana ndi kuonana maso ndi maso ndi mfumuyo?”’+ Yeremiya 52:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo gulu lankhondo la Akasidi linayamba kuthamangitsa mfumuyo+ ndipo Zedekiya anamupeza+ m’chipululu cha Yeriko. Zitatero gulu lonse lankhondo la Zedekiya linabalalika n’kumusiya yekha.+ Amosi 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Malo othawirapo munthu waliwiro adzawonongeka+ ndipo palibe munthu wamphamvu amene adzalimbe, komanso palibe munthu wamphamvu amene adzapulumutse moyo wake.+
4 ndipo Zedekiya mfumu ya Yuda sadzapulumuka m’manja mwa Akasidi, pakuti adzaperekedwa ndithu m’manja mwa mfumu ya Babulo moti adzalankhulana ndi kuonana maso ndi maso ndi mfumuyo?”’+
8 Pamenepo gulu lankhondo la Akasidi linayamba kuthamangitsa mfumuyo+ ndipo Zedekiya anamupeza+ m’chipululu cha Yeriko. Zitatero gulu lonse lankhondo la Zedekiya linabalalika n’kumusiya yekha.+
14 Malo othawirapo munthu waliwiro adzawonongeka+ ndipo palibe munthu wamphamvu amene adzalimbe, komanso palibe munthu wamphamvu amene adzapulumutse moyo wake.+