Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 15:60
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 60 Kiriyati-baala,+ kutanthauza Kiriyati-yearimu,+ ndi Raba. Mizinda iwiri ndi midzi yake.

  • Yoswa 18:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kumadzulo kwa gawolo, malirewo anakhotera kum’mwera, paphiri loyang’anizana ndi kum’mwera kwa Beti-horoni. Kuchokera pamenepo anakathera ku Kiriyati-baala, kutanthauza Kiriyati-yearimu,+ womwe ndi mzinda wa ana a Yuda. Awa ndiwo malire a kumadzulo a gawo la Benjamini.

  • 1 Samueli 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, kuchokera pamene Likasa linayamba kukhala ku Kiriyati-yearimu, panapita nthawi yaitali mpaka zinakwana zaka 20. Izi zili choncho, nyumba yonse ya Isiraeli inayamba kulirira Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena