Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 15:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kuchokera pamwamba pa phirilo, malirewo anakafika kukasupe wa madzi a Nafitoa,+ n’kupitirira mpaka kumizinda ya m’mphepete mwa phiri la Efuroni. Anapitirirabe mpaka ku Baala,+ kutanthauza Kiriyati-yearimu.+

  • Yoswa 15:60
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 60 Kiriyati-baala,+ kutanthauza Kiriyati-yearimu,+ ndi Raba. Mizinda iwiri ndi midzi yake.

  • 2 Samueli 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno Davide ndi anthu onse amene anali naye ananyamuka ndi kupita ku Baale-yuda+ kuti akatenge likasa+ la Mulungu woona. Pa likasa limeneli amaitanira dzina+ la Yehova wa makamu,+ wokhala pamwamba pa akerubi.+

  • 1 Mbiri 13:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Atatero, Davide ndi Aisiraeli onse ananyamuka kupita ku Baala,+ ku Kiriyati-yearimu, amene ali m’dera la Yuda. Anapita kumeneko kukatenga likasa la Mulungu woona, Yehova, wokhala pa akerubi.+ Palikasa limeneli, amaitanirapo dzina lake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena