Yeremiya 2:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndalanga ana anu aamuna koma sizinathandize.+ Iwo sanamve chilango* changa.+ Lupanga lanu lapha aneneri anu, ngati mkango umene ukupha anthu ambiri.+ Mateyu 23:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chotero mukudzichitira nokha umboni kuti ndinu ana a anthu amene anapha aneneri.+ 1 Atesalonika 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 amene anapha ngakhale Ambuye Yesu+ ndi aneneri+ ndi kuzunzanso ifeyo.+ Ndipo iwo sakukondweretsa Mulungu, koma akutsekereza zinthu zopindulitsa anthu onse.
30 Ndalanga ana anu aamuna koma sizinathandize.+ Iwo sanamve chilango* changa.+ Lupanga lanu lapha aneneri anu, ngati mkango umene ukupha anthu ambiri.+
15 amene anapha ngakhale Ambuye Yesu+ ndi aneneri+ ndi kuzunzanso ifeyo.+ Ndipo iwo sakukondweretsa Mulungu, koma akutsekereza zinthu zopindulitsa anthu onse.