Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 3:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Mkulu wa atsogoleri onse a Alevi anali Eleazara,+ mwana wa wansembe Aroni. Iye ndiye anali kuyang’anira onse otumikira pamalo oyera.

  • Numeri 4:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Eleazara mwana wa wansembe Aroni, aziyang’anira+ mafuta+ a nyale, zofukiza zonunkhira,+ nsembe yanthawi zonse yambewu,+ ndi mafuta odzozera.+ Aziyang’aniranso chihema chonse chopatulika ndi zonse za mmenemo, ndiwo malo oyerawo ndi ziwiya zake.”

  • Yeremiya 20:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tsopano Pasuri, mwana wa Imeri,+ wansembe, amenenso anali mtumiki wamkulu panyumba ya Yehova,+ anakhala tcheru kumvetsera pamene Yeremiya anali kulosera mwa kunena mawu amenewa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena