Numeri 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Chotero iwo ananyamuka kuphiri la Yehova,+ n’kuyenda ulendo wa masiku atatu. Likasa la pangano la Yehova+ linali patsogolo pawo ulendo wa masiku atatu wonsewo, kuwafunira malo oti amangepo msasa.+ Salimo 95:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kunena za anthu amenewa ndinalumbira mu mkwiyo wanga kuti:+“Sadzalowa mu mpumulo wanga.”+ Yesaya 63:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Monga momwe chilombo chakutchire chimatsetserekera kuchigwa, mzimu wa Yehova unawapumitsa.”+ Chotero inu munatsogolera anthu anu kuti mudzipangire dzina lokongola.+ Aheberi 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti ngati Yoswa+ anawalowetsa m’malo ampumulo,+ Mulungu sakananenanso pambuyo pake+ za tsiku lina.
33 Chotero iwo ananyamuka kuphiri la Yehova,+ n’kuyenda ulendo wa masiku atatu. Likasa la pangano la Yehova+ linali patsogolo pawo ulendo wa masiku atatu wonsewo, kuwafunira malo oti amangepo msasa.+
14 Monga momwe chilombo chakutchire chimatsetserekera kuchigwa, mzimu wa Yehova unawapumitsa.”+ Chotero inu munatsogolera anthu anu kuti mudzipangire dzina lokongola.+
8 Pakuti ngati Yoswa+ anawalowetsa m’malo ampumulo,+ Mulungu sakananenanso pambuyo pake+ za tsiku lina.