Hoseya 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndinali kuwakoka mokoma mtima ndi mwachikondi,*+ moti kwa iwo ndinakhala ngati wochotsa goli m’khosi*+ mwawo ndipo mwachikondi ndinali kubweretsera aliyense wa iwo chakudya.+
4 Ndinali kuwakoka mokoma mtima ndi mwachikondi,*+ moti kwa iwo ndinakhala ngati wochotsa goli m’khosi*+ mwawo ndipo mwachikondi ndinali kubweretsera aliyense wa iwo chakudya.+