Deuteronomo 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kodi mukupitiriza kuchitira Yehova mwa njira imeneyi,+Anthu opusa ndi opanda nzeru inu?+Kodi iye si Atate wanu amene anakulengani,+Amene anakupangani ndi kukuchititsani kukhazikika?+
6 Kodi mukupitiriza kuchitira Yehova mwa njira imeneyi,+Anthu opusa ndi opanda nzeru inu?+Kodi iye si Atate wanu amene anakulengani,+Amene anakupangani ndi kukuchititsani kukhazikika?+