Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Chotero anthu sanathe kusiyanitsa phokoso lawo losonyeza kusangalala+ ndi losonyeza kulira, chifukwa anthuwo anali kufuula kwambiri, ndipo phokoso lawo linali kumveka kutali kwambiri.

  • Salimo 126:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 126 Pamene Yehova anasonkhanitsa ndi kubwezeretsa ogwidwa ukapolo a Ziyoni,+

      Tinakhala ngati tikulota.+

  • Yesaya 51:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chotero, owomboledwa a Yehova adzabwerera ku Ziyoni ndi mfuu yachisangalalo,+ ndipo pamutu pawo padzakhala chisangalalo mpaka kalekale.+ Iwo adzapeza chisangalalo ndi chimwemwe.+ Chisoni ndi kuusa moyo zidzachoka.+

  • Ezekieli 20:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 “‘Nyumba yonse ya Isiraeli idzanditumikira m’phiri langa loyera,+ phiri lalitali la m’dziko la Isiraeli,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Kumeneko ndidzasangalala nawo ndipo ndidzafuna zopereka zanu ndi nsembe zanu za zinthu zoyambirira kucha pa zinthu zanu zonse zopatulika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena