Yesaya 58:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova azidzakutsogolerani+ nthawi zonse+ ndipo adzakukhutiritsani ngakhale m’dziko louma.+ Iye adzatsitsimula mafupa anu+ ndipo inu mudzakhala ngati munda wachinyontho chokwanira bwino,+ ndiponso ngati kasupe wamadzi yemwe madzi ake sanama.
11 Yehova azidzakutsogolerani+ nthawi zonse+ ndipo adzakukhutiritsani ngakhale m’dziko louma.+ Iye adzatsitsimula mafupa anu+ ndipo inu mudzakhala ngati munda wachinyontho chokwanira bwino,+ ndiponso ngati kasupe wamadzi yemwe madzi ake sanama.