Yeremiya 44:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ine ndikhala tcheru kuti ndiwabweretsere tsoka osati zabwino.+ Ndipo anthu onse a ku Yuda amene ali m’dziko la Iguputo adzafa ndi lupanga ndi njala yaikulu kufikira atatheratu.+ Danieli 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Inu Yehova, munakhala tcheru kuti mutigwetsere tsoka ndipo pamapeto pake munatigwetseradi tsokalo,+ pakuti inu Yehova Mulungu wathu ndinu wolungama pa ntchito zanu zonse zimene mwachita, koma ife sitinamvere mawu anu.+
27 Ine ndikhala tcheru kuti ndiwabweretsere tsoka osati zabwino.+ Ndipo anthu onse a ku Yuda amene ali m’dziko la Iguputo adzafa ndi lupanga ndi njala yaikulu kufikira atatheratu.+
14 “Inu Yehova, munakhala tcheru kuti mutigwetsere tsoka ndipo pamapeto pake munatigwetseradi tsokalo,+ pakuti inu Yehova Mulungu wathu ndinu wolungama pa ntchito zanu zonse zimene mwachita, koma ife sitinamvere mawu anu.+