Yeremiya 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi iliyonse imene ndinganene kuti ndizula, kugwetsa ndi kuwononga mtundu uliwonse wa anthu kapena ufumu,+ Yeremiya 45:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Umuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Taona! Zimene ndamanga, ndikuzigwetsa, ndipo zimene ndabzala, ndikuzizula. Ndichita zimenezi m’dziko lonse.+
7 Pa nthawi iliyonse imene ndinganene kuti ndizula, kugwetsa ndi kuwononga mtundu uliwonse wa anthu kapena ufumu,+
4 “Umuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Taona! Zimene ndamanga, ndikuzigwetsa, ndipo zimene ndabzala, ndikuzizula. Ndichita zimenezi m’dziko lonse.+