Yesaya 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano amuna inu, ndikuuzani zimene ndichite ndi munda wanga wa mpesa: Ndichotsa zomera zimene zinali ngati mpanda wa mundawo,+ ndipo ndiutentha.+ Ndigumula mpanda wake wamiyala ndipo mundawo udzangokhala malo oti azipondapondapo.+ Yeremiya 31:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Monga mmene ndakhalira ndikufunafuna mpata+ kuti ndiwazule, kuwagwetsa, kuwapasula, kuwawononga ndi kuwasakaza,+ ndidzakhalanso nawo tcheru kuti ndiwamange ndi kuwabzala,”+ watero Yehova.
5 Tsopano amuna inu, ndikuuzani zimene ndichite ndi munda wanga wa mpesa: Ndichotsa zomera zimene zinali ngati mpanda wa mundawo,+ ndipo ndiutentha.+ Ndigumula mpanda wake wamiyala ndipo mundawo udzangokhala malo oti azipondapondapo.+
28 “Monga mmene ndakhalira ndikufunafuna mpata+ kuti ndiwazule, kuwagwetsa, kuwapasula, kuwawononga ndi kuwasakaza,+ ndidzakhalanso nawo tcheru kuti ndiwamange ndi kuwabzala,”+ watero Yehova.