Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 26:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Vinyoyu akuimira+ ‘magazi+ anga a pangano,’+ amene adzakhetsedwa chifukwa cha anthu ambiri+ kuti machimo akhululukidwe.+

  • Maliko 14:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndiyeno anawauza kuti: “Vinyoyu akuimira ‘magazi+ anga a pangano,’+ amene adzakhetsedwa+ chifukwa cha anthu ambiri.+

  • Luka 22:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Anachitanso chimodzimodzi ndi kapu+ atadya chakudya chamadzulocho. Iye anati: “Kapu iyi ikutanthauza pangano latsopano+ pamaziko a magazi anga,+ amene adzakhetsedwa chifukwa cha inu.+

  • 1 Akorinto 11:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Anachitanso chimodzimodzi ndi kapu+ atadya chakudya chamadzulo, ndipo anati: “Kapu iyi ikutanthauza pangano latsopano+ pamaziko a magazi anga.+ Muzichita zimenezi nthawi zonse pamene mukumwa za m’kapu imeneyi pondikumbukira.”+

  • Aheberi 8:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pakuti iye akuimba anthu mlandu pamene akunena kuti: “‘Taonani! Masiku adzafika, pamene ndidzachita pangano latsopano ndi nyumba ya Isiraeli komanso ndi nyumba ya Yuda,’ watero Yehova.+

  • Aheberi 10:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “‘Pangano limene ndidzapanga nawo pambuyo pa pangano loyamba lija ndi ili: Ndidzaika malamulo anga m’mitima yawo ndi kuwalemba m’maganizo mwawo,’ watero Yehova,”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena