Yesaya 51:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ambuye wako, Yehova, Mulungu wako, amene amateteza+ anthu ake, wanena kuti: “Taona! Ine ndidzachotsa m’manja mwako chikho chochititsa munthu kudzandira.+ Sudzamwanso chipanda, chikho cha mkwiyo wanga.+
22 Ambuye wako, Yehova, Mulungu wako, amene amateteza+ anthu ake, wanena kuti: “Taona! Ine ndidzachotsa m’manja mwako chikho chochititsa munthu kudzandira.+ Sudzamwanso chipanda, chikho cha mkwiyo wanga.+