Yesaya 54:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Kwa ine, zimenezi zili ngati masiku a Nowa.+ Monga mmene ndinalumbirira kuti madzi a Nowa sadzadutsanso padziko lapansi,+ momwemonso ndalumbira kuti sindidzakukwiyira kapena kukudzudzula.+ Yesaya 62:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova walumbira ndi dzanja lake lamanja+ ndiponso ndi mkono wake wamphamvu+ kuti: “Sindidzaperekanso mbewu zanu kwa adani anu ngati chakudya,+ ndipo alendo sadzamwanso vinyo wanu watsopano+ amene munachita kumuvutikira.
9 “Kwa ine, zimenezi zili ngati masiku a Nowa.+ Monga mmene ndinalumbirira kuti madzi a Nowa sadzadutsanso padziko lapansi,+ momwemonso ndalumbira kuti sindidzakukwiyira kapena kukudzudzula.+
8 Yehova walumbira ndi dzanja lake lamanja+ ndiponso ndi mkono wake wamphamvu+ kuti: “Sindidzaperekanso mbewu zanu kwa adani anu ngati chakudya,+ ndipo alendo sadzamwanso vinyo wanu watsopano+ amene munachita kumuvutikira.