Yeremiya 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Pita ukauze Zedekiya mfumu ya Yuda,+ kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Ine ndikupereka mzinda uwu m’manja mwa mfumu ya Babulo+ ndipo idzautentha.+ Yeremiya 37:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo Akasidi adzabweranso ndithu kudzamenyana ndi mzinda uno, kuulanda ndi kuutentha ndi moto.”+
2 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Pita ukauze Zedekiya mfumu ya Yuda,+ kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Ine ndikupereka mzinda uwu m’manja mwa mfumu ya Babulo+ ndipo idzautentha.+